Sanitary Napkin ndi chinthu chofewa chomwe mkazi amavala kuti atenge magazi pa nthawi yomwe ali ndi kusamba (=kutuluka magazi mwezi uliwonse).